Jeremiah 35:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tangokhala m'mahema basi. Motero tamvera ndi kusunga malamulo onse a kholo lathu Yonadabu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma takhala m'mahema, ntimvera, ntichita monga mwa zonse anatiuza Yonadabu kholo lathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma takhala mʼmatenti ndipo tamvera kwathunthu chilichonse chimene kholo lathu Yehonadabu anatilamula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma takhala m'mahema, ntimvera, nticita monga mwa zonse anatiuza Yonadabu kholo lathu.