Jeremiah 35:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
tsono Chauta Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israele, akunena kuti, ‘Yonadabu mwana wa Rekabu sadzasoŵa mdzukulu wonditumikira mpaka muyaya.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele: Yonadabu mwana wa Rekabu sadzasowa munthu wakuima pamaso panga kumuyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli akuti, “Yehonadabu mwana wa Rekabu sadzasowa munthu wonditumikira Ine nthawi zonse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Yonadabu mwana wa Rekabu sadzasowa munthu wakuima pamaso panga kumuyaya.