Jeremiah 35:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndidabwera ndi Yazaniya (mwana wa Yeremiya winanso, mwana wa Habaziniya,) pamodzi ndi abale ake ndiponso ana ake onse aamuna, ndiye kuti banja lonse la Arekabu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinatenga Yazaniya mwana wa Yeremiya, mwana wa Habaziniya, ndi abale ake, ndi ana amuna ake, ndi nyumba yonse ya Arekabu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ndinakatenga Yaazaniya (mwana wa Yeremiya winanso amene anali mwana wa Habaziniya), abale ake, ana ake onse aamuna ndi banja lonse la Arekabu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinatenga Yaasaniya mwana wa Yeremiya, mwana wa Habazinya, ndi abale ace, ndi ana amuna ace, ndi nyumba yonse ya Arekabu;