Jeremiah 35:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sitidamange nyumba kuti tizikhalamo, kapena kulima minda yamphesa kapena minda ina iliyonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngakhale kudzimangira nyumba zokhalamo; ndipo sitili nao munda wamphesa, kapena munda, kapena mbeu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kapena kumanga nyumba kuti tizikhalamo kapenanso kukhala ndi minda ya mpesa, minda ina iliyonse kapena mbewu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ngakhale kudzimangira nyumba zokhalamo; ndipo sitiri nao munda wamphesa, kapena munda, kapena mbeu;