Jeremiah 36:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono onse ataloŵa m'Nyumba ya Chauta, Baruki adaŵerenga mau a Chauta olembedwa m'buku aja, anthu onse alikumva. Adaŵerengera m'chipinda cha Gemariya, mwana wa mlembi Safani, chimene chinali m'bwalo lapamwamba, pafupi ndi Chipata Chatsopano choloŵera ku Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Baruki anawerenga m'buku mau a Yeremiya m'nyumba ya Yehova, m'chipinda cha Gemariya mwana wa Safani mlembi, m'bwalo la kumtunda, pa khomo la chipata chatsopano cha nyumba ya Yehova, m'makutu a anthu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atayima pa chipinda cha Gemariya mwana wa mlembi Safani, chimene chinali mʼbwalo lapamwamba, pafupi ndi Chipata Chatsopano cholowera ku Nyumba ya Yehova, Baruki anawerenga mawu onse a Yeremiya amene anali mʼbuku muja kwa anthu onse amene anali ku Nyumba ya Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Baruki anawerenga m'buku mau a Yeremiya m'nyumba ya Yehova, m'cipinda ca Gemariya mwana wa Safani mlembi, m'bwalo la kumtunda, pa khomo la cipata catsopano ca nyumba ya Yehova, m'makutu a anthu onse.