Jeremiah 36:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mikaya mwana wa Gemariya, mdzukulu wa Safani, atamva mau onse a Chauta olembedwa m'buku aja,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Mikaya mwana wa Gemariya, mwana wa Safani, anamva m'buku mau onse a Yehova,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikaya mwana wa Gemariya, mwana wa Safani, atamva mawu onse a Yehova ochokera mʼbukumo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Mikaya mwana wa Hemariya, mwana wa Safani, anamva m'buku mau onse a Yehova,