Jeremiah 36:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tenga buku ndipo ulembepo mau onse amene ndalankhula nawe za Israele ndi Yuda ndi za mitundu yonse ya anthu, kuyambira tsiku limene ndidalankhula nawe nthaŵi ya Yosiya mpaka lero lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tenga buku lampukutu, nulembe m'menemo mau onse ndanena kwa iwe akunenera Israele, ndi akunenera Yuda, ndi akunenera amitundu onse kuyambira tsiku ndinanena kwa iwe, kuyambira masiku a Yosiya, mpaka lero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tenga buku ndipo ulembemo mawu onse amene ndayankhula nawe otsutsa Israeli, Yuda ndi mitundu yonse ya anthu, kuyambira nthawi imene ndinayamba kuyankhula nawe pa nthawi ya ulamuliro wa Yosiya mpaka lero lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tenga buku lampukutu, nulembe m'menemo mau onse ndanena kwa iwe akunenera Israyeli, ndi akunenera Yuda, ndi akunenera amitundu onse, kuyambira tsiku ndinanena kwa iwe, kuyambira masiku a Yosiya, mpaka lero.