Jeremiah 36:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Unali mwezi wachisanu ndi chinai ndipo mfumu inali m'nyumba ya pa nyengo yachisanu, ikuwotha moto umene ankasonkha chifukwa cha kuzizira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu anakhala m'nyumba ya nyengo yachisanu mwezi wachisanu ndi chinai; ndipo munali moto m'mbaula pamaso pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Unali mwezi wachisanu ndi chinayi ndipo mfumu inali mʼnyumba ya pa nyengo yozizira, ikuwotha moto umene anasonkha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu anakhala m'nyumba ya nyengo yacisanu mwezi wacisanu ndi cinai; ndipo munali moto m'nkhumbaliro pamaso pace.