Jeremiah 36:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe mfumu kapena wina aliyense mwa aphungu ake amene adamva mau ameneŵa, sadachite mantha kapena kung'amba zovala zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo sanaope, sanang'ambe nsalu zao, kapena mfumu, kapena atumiki ake aliyense amene anamva mau onsewa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu pamodzi ndi omutumikira ake onse amene anamva mawu onsewa sanachite mantha kapena kungʼamba zovala zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo sanaopa, sanang'ambe nsaru zao, kapena mfumu, kapena atumiki ace ali yense amene anamva mau onsewa.