Jeremiah 36:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo pamene Elinatani, Delaya ndi Gemariya adapempha mfumu kuti isatenthe bukulo, iyoyo sidaŵamvere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsononso Elinatani ndi Delaya ndi Gemariya anapembedzera mfumu kuti asatenthe mpukutuwo; koma anakana kumvera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale kuti Elinatani, Delaya, ndi Gemariya anapempha mfumu kuti isatenthe bukulo, mfumuyo sinawamvere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsononso Elinatani ndi Deliya ndi Gemariya anapembedzera mfumu kuti asatenthe mpukutuwo; koma anakana kumvera.