Jeremiah 36:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mwina mwake adzapemba kwa Chauta, ndipo munthu aliyense adzasiya makhalidwe ake oipa. Ndithu Chauta waŵakwiyira anthu ameneŵa, ukali wake ndi woyaka kwabasi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kapena pembedzero lao lidzagwa pamaso pa Yehova, ndipo adzabwerera yense kuleka njira yake yoipa; pakuti mkwiyo ndi ukali umene Yehova wanenera anthu awa ndi waukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwina mwake adzapempha kwa Yehova ndipo aliyense adzatembenuka ndi kusiya makhalidwe ake oyipa pakuti mkwiyo ndi ukali wa Yehova pa anthu awa ndi woopsa kwambiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena pembedzero lao lidzagwa pamaso pa Yehova, ndipo adzabwerera yense kuleka njira yace yoipa; pakuti mkwiyo ndi ukali umene Yehova wanenera anthu awa ndi waukuru.