Jeremiah 37:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nebukadinezara, mfumu ya ku Babiloni, adakhazika Zedekiya pa mpando waufumu wa ku Yuda, kuloŵa m'malo mwa Yehoyakini mwana wa Yehoyakimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Zedekiya mwana wa Yosiya anakhala mfumu m'malo a Koniya mwana wa Yehoyakimu, amene Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni inamlowetsa mfumu m'dziko la Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nebukadinezara mfumu ya Babuloni, inakhazika pa mpando waufumu Zedekiya mwana wa Yosiya kukhala mfumu ya Yuda. Iye analowa mʼmalo mwa Yehoyakini mwana wa Yehoyakimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Zedekiya mwana wa Yosiya anakhala mfumu m'malo a Koniya mwana wa Yehoyakimu, amene Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo inamlowetsa mfumu m'dziko la Yuda.