Jeremiah 37:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yeremiya adanyamuka kuchoka ku Yerusalemu kupita ku dziko la Benjamini kuti akalandire gawo lake la minda ya makolo ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo Yeremiya anatuluka m'Yerusalemu kumuka kudziko la Benjamini, kukalandira gawo lake kumeneko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yeremiya ananyamuka kuchoka ku Yerusalemu ndi kumapita ku dziko la Benjamini kuti akalandire gawo lake la minda ya makolo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo Yeremiya anaturuka m'Yerusalemu kumuka ku dziko la Benjamini, kukalandira gawo lace kumeneko.