Jeremiah 37:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yeremiya adaikidwa m'ndende ya pansi pa nthaka, nakhala m'menemo nthaŵi yaitali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atafika Yeremiya kunyumba yadzenje, ku tizipinda take nakhalako Yeremiya masiku ambiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yeremiya anayikidwa mʼndende ya pansi pa nthaka, kumene anakhalako nthawi yayitali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atafika Yeremiya ku nyumba yadzenje, ku tizipinda tace nakhalako Yeremiya masiku ambiri;