Jeremiah 37:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ali kuti aneneri anu aja amene adakuloserani kuti mfumu ya ku Babiloni sidzakuthirani nkhondo inuyo ndi dziko lanu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsopano ali kuti aneneri anu, amene ananenera inu, kuti, Mfumu ya ku Babiloni sidzakudzerani inu, kapena dziko lino?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ali kuti aneneri anu amene anakuloserani kuti, ‘Mfumu ya ku Babuloni sidzakuthirani nkhondo pamodzi ndi dziko lino’?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsopano ali kuti aneneri anu, amene ananenera inu, kuti, Mfumu ya ku Babulo sidzakudzerani inu, kapena dziko lino?