Jeremiah 37:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Zedekiyayo ndi aphungu ake, pamodzi ndi anthu onse a m'dzikomo, sadamvere mau amene Chauta adalankhula kudzera mwa mneneri Yeremiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngakhale iye, ngakhale atumiki ake, ngakhale anthu a padziko, sanamvere mau a Yehova, amene ananena mwa Yeremiya mneneri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Zedekiya kapena atumiki ake ngakhalenso anthu a mʼdzikomo sanasamalire mawu a Yehova amene anayankhula kudzera mwa mneneri Yeremiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngakhale iye, ngakhale atumiki ace, ngakhale anthu a padziko, sanamvere mau a Yehova, amene ananena mwa Yeremiya mneneri.