Jeremiah 37:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndikukupemphani inu mfumu mbuyanga, kuti mumve pempho langa. Musandibwezere ku nyumba ya mlembi Yonatani, kuwopa kuti ndingakafereko.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsopano tamvanitu, mbuyanga mfumu; pembedzero langa ligwe pamaso panu; kuti musandibwezere kunyumba ya Yonatani mlembi, ndingafe kumeneko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsopano, mbuye wanga mfumu, chonde tamverani. Loleni ndinene pempho langa pamaso panu: Musandibwezere ku nyumba ya mlembi Yonatani, kuopa kuti ndingakafere kumeneko.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsopano tamvanitu, mbuyanga mfumu; pembedzero langa ligwe pamaso panu; kuti musandibwezere ku nyumba ya Yonatani mlembi, ndingafe kumeneko.