Jeremiah 37:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi imeneyo nkuti Yeremiya asanaponyedwe m'ndende, choncho anali ndi ufulu wotha kuyenda pakati pa anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yeremiya analikuyendayenda mwa anthu; chifukwa asanamuike iye m'nyumba yandende.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi imeneyinso nʼkuti Yeremiya ali ndi ufulu woyenda pakati pa anthu chifukwa anali asanaponyedwe mʼndende.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yeremiya analikuyendayenda mwa anthu; cifukwa asanamuike iye m'nyumba yandende.