Jeremiah 38:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Sefatiya mwana wa Matani, Gedaliya mwana wa Pasuri, Yukala mwana wa Selemiya, ndi Pasuri mwana wa Malakiya, adamva zimene Yeremiya ankauza anthu zoti
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Sefatiya mwana wa Matani ndi Gedaliya mwana wa Pusuri, ndi Yukala mwana wa Selemiya, ndi Pasuri mwana wa Malikiya, anamva mau amene Yeremiya ananena ndi anthu onse, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sefatiya mwana wa Matani, Gedaliya mwana wa Pasi-Huri, Yukali mwana wa Selemiya, ndi Pasi-Huri mwana wa Malikiya anamva zimene Yeremiya ankawuza anthu onse kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sefatiya mwana wa Matani ndi Gedaliya mwana wa Pusuri, ndi Yukali mwana wa Selemiya, ndi Pasuri mwana wa Malikiya, anamva mau amene Yeremiya ananena ndi anthu onse, kuti,