Jeremiah 38:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo mwachinsinsi mfumu Zedekiya adalumbira pamaso pa Yeremiya kuti, “Pali Chauta wamoyo amene adatipatsa moyo, ine sindikupha. Ndipo sindikupereka kwa anthu amene afuna kukuphaŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu Zedekiya analumbira m'tseri kwa Yeremiya, kuti, Pali Yehova, amene anatilengera ife moyo uno, sindidzakupha iwe sindidzakupereka iwe m'manja mwa anthu awa amene afuna moyo wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mfumu Zedekiya mwachinsinsi inalumbira kwa Yeremiya kuti, “Pali Yehova wamoyo, amene amatipatsa moyo, sindidzakupha ngakhalenso kukupereka kwa amene akufuna kukuphawa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Zedekiya analumbira m'tseri kwa Yeremiya, kuti, Pali Yehova, amene anatilengera ife moyo uno, sindidzakupha iwe sindidzakupereka iwe m'manja mwa anthu awa amene afuna moyo wako.