Jeremiah 38:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mukakana kutuluka kuti mukadzipereke, Chauta wandiwululira kuti
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati mukana kutuluka, mau anandisonyeza Yehova ndi awa:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mukakana kudzipereka, chimene Yehova wandiwululira ndi ichi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati mukana kuturuka, mau anandisonyeza Yehova ndi awa: