Jeremiah 38:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono udzaŵayankhe kuti, ‘Ndinalikupempha kwa amfumu kuti asandibwezenso ku nyumba ya Yonatani, kuti ndikafe kumeneko.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo uziti kwa iwo, Ndinagwa ndi pembedzero langa pamaso pa mfumu, kuti asandibwezerenso kunyumba ya Yonatani ndifere komweko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
udzawawuze kuti, ‘Ine ndimapempha mfumu kuti isandibwezerenso ku nyumba ya Yonatani kuti ndikafere kumeneko.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo uziti kwa iwo, Ndinagwa ndi pembedzero langa pamaso pa mfumu, kuti asandibwezerenso ku nyumba ya Yonatani ndifere komweko.