Jeremiah 38:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mzinda uno udzaperekedwadi kwa ankhondo a mfumu ya ku Babiloni, ndipo adzaulanda.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova atero, Mudziwu udzapatsidwatu m'dzanja la nkhondo ya mfumu ya ku Babiloni, ndipo adzaulanda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mzinda uno udzaperekedwa ndithu kwa gulu lankhondo la mfumu ya ku Babuloni, amene adzawulande.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova atero, Mudziwu udzapatsidwatu m'dzanja la nkhondo ya mfumu ya ku Babulo, ndipo adzaulanda.