Jeremiah 38:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu Zedekiya adati, “Suyu, ali m'manja mwanu. Ine mfumu sindingakuletseni ai.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu Zedekiya anati, Taonani, ali m'manja mwanu; pakuti mfumu singathe kuchita kanthu kotsutsana nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Zedekiya anayankha kuti, “Munthuyu ali mʼmanja mwanu. Ine sindingakuletseni chimene mukufuna kumuchitira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu Zedekiya anati, Taonani, ali m'manja mwanu; pakuti mfumu singathe kucita kanthu kotsutsana nanu.