Jeremiah 38:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ebedemeleki adatuluka ku nyumba ya mfumu kukaiwuza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ebedemeleki anatuluka m'nyumba ya mfumu, nanena ndi mfumu, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ebedi-Meleki anatuluka ku nyumba ya mfumu kukayiwuza kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ebedi-Meleki anaturuka m'nyumba ya mfumu, nanena ndi mfumu, kuti,