Jeremiah 39:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adalankhula ndi Yeremiya pamene anali m'ndende ku bwalo la alonda. Adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yeremiya, potsekeredwa iye m'bwalo la kaidi, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yeremiya ali mʼndende ku bwalo la alonda, Yehova anayankhula naye:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yeremiya, potsekeredwa iye m'bwalo la kaidi, kuti,