Jeremiah 39:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu ndidzakupulumutsa, ndipo sudzaphedwa pa nkhondo. Udzapulumuka chifukwa choti wandikhulupirira,’ ” akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndidzakupulumutsatu ndipo sudzagwa ndi lupanga, koma udzakhala nao moyo wako ngati chofunkha, pakuti wandikhulupirira Ine, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithu ndidzakupulumutsa; sudzaphedwa pa nkhondo koma udzapulumuka, chifukwa wadalira Ine, akutero Yehova.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndidzakupulumutsatu ndipo sudzagwa ndi lupanga, koma udzakhala nao moyo wako ngati cofunkha, pakuti wandikhulupirira Ine, ati Yehova.