Jeremiah 39:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka chakhumi ndi chimodzi cha ufumu wa Zedekiya, mwezi wachinai, tsiku lachisanu ndi chinai la mweziwo, malinga a mzindawo adabooledwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chakhumi ndi chimodzi cha Zedekiya, mwezi wachinai, tsiku lachisanu ndi chinai, mudzi unabooledwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pa tsiku lachisanu ndi chinayi la mwezi wachinayi wa chaka cha khumi ndi chimodzi cha Zedekiya, malinga a mzindawo anabowoledwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cakhumi ndi cimodzi ca Zedekiya, mwezi wacinai, tsiku lacisanu ndi cinai, mudzi unabooledwa.