Jeremiah 39:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu ya ku Babiloni idapha ana aamuna a Zedekiya ku Ribula, iyeyo akuwona. Idaphanso atsogoleri onse a ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mfumu ya ku Babiloni inapha ana a Zedekiya ku Ribula pamaso pake; mfumu ya ku Babiloni niphanso aufulu onse a Yuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ku Ribulako, mfumu ya ku Babuloni inapha ana aamuna a Zedekiya iyeyo akuona. Inaphanso anthu olemekezeka onse a ku Yuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mfumu ya ku Babulo inapha ana a Zedekiya ku Ribila pamaso pace; mfumu ya ku Babulo niphanso aufulu onse a Yuda.