Jeremiah 39:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ababiloni adatentha nyumba yaufumu, Nyumba ya Chauta pamodzi ndi nyumba zina zonse za anthu. Ndipo adagwetsa malinga a Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ababiloni anatentha ndi moto nyumba ya mfumu, ndi nyumba za anthu, nagumula malinga a Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ababuloni anatentha nyumba ya mfumu ndi nyumba za anthu, ndiponso anagwetsa malinga a Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Akasidi anatentha ndi moto nyumba ya mfumu, ndi nyumba za anthu, nagumula malinga a Yerusalemu.