Jeremiah 40:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu adayankha Yohanani mwana wa Kareya kuti, “Iyai, usachite zotero. Zimene ukunena za Ismaele nzabodza.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu anati kwa Yohanani mwana wa Kareya, Usachite ichi; pakuti unamizira Ismaele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu anawuza Yohanani mwana wa Kareya kuti, “Usachite zimenezo! Zimene ukunena za Ismaeli ndi zabodza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu anati kwa Yohanani mwana wa Kareya, Usacite ici; pakuti unamizira Ismayeli.