Jeremiah 41:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yohanani, mwana wa Kareya, ndi atsogoleri a ankhondo, adamva zoipa zimene Ismaele mwana wa Netaniya adaachita,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pamene Yohanani mwana wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo akhala naye, anamva zoipa zonse anazichita Ismaele mwana wa Netaniya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Yohanani mwana wa Kareya ndi atsogoleri onse a ankhondo amene anali naye pamodzi anamva zoyipa zonse zimene Ismaeli mwana wa Netaniya anachita,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pamene Yohanani mwana wa Kareya, ndi akazembe Onse a nkhondo akhala naye, anamva zoipa zonse anazicita Ismayeli mwana wa Netaniya,