Jeremiah 41:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
adasonkhanitsa anthu onse amene anali nawo, napita kukamenyana naye nkhondo. Adakampeza ku chidziŵe cha ku Gibiyoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
anatenga anthu onse, nanka kukamenyena ndi Ismaele mwana wa Netaniya, nampeza pa madzi ambiri a m'Gibiyoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anatenga ankhondo awo onse kupita kukamenyana ndi Ismaeli mwana wa Netaniya. Anakamupeza kufupi ndi chidziwe chachikulu cha ku Gibiyoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
anatenga anthu onse, nanka kukamenyana ndi Ismayeli mwana wa Netaniya, nampeza pa madzi ambiri a m'Gibeoni.