Jeremiah 41:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo anthu onse amene Ismaele adaaŵagwira ataona Yohanani mwana wa Kareya ndi atsogoleri a magulu ankhondo aja, adasangalala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali pamene anthu onse amene anali ndi Ismaele anaona Yohanani mwana wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo okhala naye, anasekera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene anthu onse amene Ismaeli anawagwira anaona Yohanani mwana wa Kareya pamodzi ndi atsogoleri a ankhondo amene anali naye, anasangalala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali pamene anthu onse amene anali ndi Ismayeli anaona Yohanani mwana wa Kareya, ndi akazembe onse a nkhondo okhala naye, anasekera.