Jeremiah 41:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atangofika pakati pa mudzi, Ismaele mwana wa Netaniya ndi anthu ake, adaŵapha onsewo naŵataya m'chitsime.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali, pamene analowa pakati pa mudzi, Ismaele mwana wa Netaniya anawapha, nawaponya pakati pa dzenje, iye ndi anthu okhala naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atafika pakati pa mzinda, Ismaeli mwana wa Netaniya pamodzi ndi anthu amene anali naye anawapha anthuwo ndi kuwaponya mʼchitsime.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali, pamene analowa pakati pa mudzi, Ismayeli mwana, wa Netaniya anawapha, nawaponya pakati pa dzenje, iye ndi anthu okhala naye.