Jeremiah 43:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onsewo adapita nawo ku Ejipito monyoza mau a Chauta, nakafika ku Tapanesi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anadza nalowa m'dziko la Ejipito; pakuti sanamvere mau a Yehova; ndipo anadza mpaka ku Tapanesi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero anthuwo analowa mʼdziko la Igupto chifukwa anakana kumvera Yehova, nakafika ku Tapanesi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anadza nalowa m'dziko la Aigupto; pakuti sanamvera mau a Yehova; ndipo anadza mpaka ku Tapanesi.