Jeremiah 44:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atalimva yankho la anthu onsewo, amuna ndi akazi omwe, Yeremiya adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yeremiya anati kwa anthu onse, kwa amuna, ndi kwa akazi, kwa anthu onse amene anambwezera mau amenewa, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yeremiya atamva kuyankha kumeneku anawawuza kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yeremiya anati kwa anthu onse, kwa amuna, ndi kwa akazi, kwa anthu onse amene anambwezera mau amenewa, ndi kuti,