Jeremiah 45:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naŵa mau amene mneneri Yeremiya adalembetsa Baruki mwana wa Neriya m'buku, chaka chachinai cha ufumu wa Yehoyakimu mwana wa Yosiya mfumu ya ku Yuda:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau amene ananena Yeremiya mneneri kwa Baruki mwana wake wa Neriya, pamene analemba mau awa m'buku ponena Yeremiya, chaka chachinai cha Yehoyakimu mwana wake wa Yosiya, mfumu ya Yuda, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uwu ndi uthenga umene mneneri Yeremiya anawuza Baruki mwana wa Neriya mʼchaka cha chinayi cha Yehoyakimu mwana wa mwana ya Yosiya kuti alembe mʼbuku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau amene ananena Yeremiya mneneri kwa Baruki mwana wace wa Neriya, pamene analemba mau awa m'buku ponena Yeremiya, caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, ndi kuti,