Jeremiah 45:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandiwuza kuti ndilankhule mau aŵa kwa iwe Baruki, ‘Chimene ndidamanga, ndikuchigwetsa. Chimene ndidabzala, ndikuchizula. Umu ndi m'mene ndidzachitire ndi dziko lonse lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uzitero naye, Yehova atero: Taonani, chimene ndamanga ndidzapasula, ndi chimene ndaoka ndidzazula; ndidzatero m'dziko lonseli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova akukuwuza kuti, “Ndidzagwetsa chimene ndinamanga ndipo ndidzazula chimene ndinadzala. Ndidzachita zimenezi mʼdziko lonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uzitero naye, Yehova atero: Taonani, cimene ndamanga ndidzapasula, ndi cimene ndaoka ndidzazula; ndidzatero m'dziko lonseli.