Jeremiah 47:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzamva mgugu wa akavalo othamanga, adzamva phokoso la magaleta ake, ndi kulira kwa mikombero yake. Atate sadzaganizirako za ana ao, adzangokhala ali manja lende!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomveka migugu ya ziboda za olimba ake, pogumukira magaleta ake, ndi pophokosera njinga zake, atate sadzacheukira ana ao chifukwa cha kulefuka kwa manja ao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
akadzamva mgugu wa ngʼombe zazimuna zothamanga, phokoso la magaleta ake ndi kulira kwa mikombero yake. Makolo sadzatembenuka kuti athandize ana awo; manja awo adzangoti khoba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomveka migugu ya ziboda za olimba ane, pogumukira magareta ace, ndi pophokosera njinga zace, atate sadzaceukira ana ao cifukwa ca kulefuka kwa manja ao;