Jeremiah 47:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi lupangalo lingapumule bwanji pamene Chauta walipatsa kale ntchito yoti limchitire? Walituma kuti likalimbane ndi Asikeloni, kuti likathire nkhondo anthu a m'mbali mwa nyanja.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzakhala chete bwanji, popeza Yehova anakulangiza? Za Asikeloni, ndi za m'mphepete mwa nyanja, pamenepo analiika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma lupangalo lidzapumula bwanji pamene Yehova walilamulira kuti lithire nkhondo Asikeloni ndi anthu a mʼmbali mwa nyanja?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzakhala cete bwanji, popeza Yehova anakulangiza? za Asikeloni, ndi za m'mbali mwa nyanja, pamenepo analiika.