Jeremiah 48:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndi wotembereredwa amene amagwira ntchito ya Chauta mwaulesi. Ndi wotembereredwa amene amaletsa lupanga lake kutema ndi kupha anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atembereredwe iye amene agwira ntchito ya Yehova monyenga, atembereredwe iye amene abweza lupanga lake kumwazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Wotembereredwa munthu amene amagwira ntchito ya Yehova monyinyirika! Wotembereredwa munthu amene amaletsa lupanga lake kupha anthu!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atembereredwe iye amene agwira nchito ya Yehova monyenga, atembereredwe iye amene abweza lupanga lace kumwazi.