Jeremiah 48:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Mowabu adzachita manyazi ndi Kemosi, mulungu wake, monga momwe Israele adachitira naye manyazi Betele, mulungu amene ankamukhulupirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mowabu adzachita manyazi chifukwa cha Kemosi, monga nyumba ya Israele inachita manyazi chifukwa cha Betele amene anamkhulupirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Mowabu adzachita manyazi ndi Kemosi, monga momwe Aisraeli anachitira manyazi ndi Beteli amene ankamukhutulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Moabu adzacita manyazi cifukwa ca Kemosi, monga nyumba ya Israyeli inacita manyazi cifukwa ca Beteli amene anamkhulupirira,