Jeremiah 48:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kugwa kwa Mowabu kuli pafupi. Chiwonongeko changokhala pang'onong'ono kuti chimugwere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka la Mowabu layandikira kudza, nsautso yake ifulumiratu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kugwa kwa Mowabu kuli pafupi; masautso ake akubwera posachedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka la Moabu layandikira kudza, nsautso yace ifulumiratu.