Jeremiah 48:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu amene mumakhala ku Aroere, imani m'mbali mwa mseu muziwonerera. Mufunse mwamuna amene wathaŵa ndiponso mkazi amene wapulumuka, munene kuti, ‘Kodi kwagwanji?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe wokhala m'Aroere, ima panjira, nusuzumire umfunse iye amene athawa, ndi mkazi amene apulumuka; nuti, Chachitidwa chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu amene mumakhala ku Aroeri, imani mʼmbali mwa msewu ndi kumaonerera. Funsani mwamuna amene akuthawa ndiponso mkazi amene wapulumuka, afunseni kuti, ‘Kodi chachitika nʼchiyani?’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe wokhala m'Aroeri, ima panjira, nusuzumire umfunse iye amene athawa, ndi mkazi amene apulumuka; nuti, Cacitidwa ciani?