Jeremiah 48:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chiweruzo chafika ku dziko lakumapiri, ndiye kuti mizinda iyi: Holoni, Yaza, Mefati
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chiweruzo chafika pa dziko lachidikha; pa Holoni, ndi pa Yahazi, ndi pa Mefaati;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiweruzo chabwera ku mizinda ya ku mapiri, ndiyo Holoni, Yaza, Mefaati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ciweruzo cafika pa dziko lacidikha; pa Holoni, ndi pa Yaza, ndi pa Mefati;