Jeremiah 48:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Keriyoti, Bozira ndi mizinda yonse ya ku Mowabu, yakutali ndi yakufupi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi pa Keriyoti, ndi pa Bozira, ndi pa midzi yonse ya dziko la Mowabu, yakutali kapena yakufupi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Keriyoti ndi Bozira ndi mizinda yonse ya Mowabu, yakutali ndi yapafupi yomwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi pa Kerioti, ndi pa Bozira, ndi pa midzi yonse ya dziko la Moabu, yakutari kapena yakufupi.