Jeremiah 48:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Imvani kulira kwachisoni kwa anthu a ku Horonaimu, akuti, ‘Chisakazo ndi chiwonongeko chachikulutu!’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau amveka kuchokera ku Horonaimu, kufunkha ndi kuononga kwakukulu!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tamvani mfuwu wa anthu a ku Horonaimu. Iwo akulira kuti, ‘Kusakazika ndi kuwonongeka kwakukulu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau amveka kucokera ku Horonaimu, kufunkha ndi kuononga kwakukuru!