Jeremiah 48:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikudziŵa kudzikuza kwake. Mau ake odzitama ngachabechabe, ntchito zake nzopanda pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndidziwa mkwiyo wake, ati Yehova, kuti uli chabe; zonyenga zake sizinachita kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikuzidziwa ntchito zake, akutero Yehova. Ntchitozo ndi nʼzosapindulitsa kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndidziwa mkwiyo wace, ati Yehova, kuti uli cabe; zonyenga zace sizinacita kanthu.