Jeremiah 48:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndikulira chifukwa cha Mowabu. Ndikulira mwachisoni chifukwa cha anthu onse a ku Mowabu. Ndikulira anthu a ku Kiriheresi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ndidzakuwira Mowabu; inde, ndidzafuulira Mowabu yense, adzalirira anthu a ku Kiriheresi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake ndidzamulira Mowabu, ine ndikulira chifukwa cha anthu onse a ku Mowabu, ndikubuwula chifukwa cha anthu a ku Kiri Heresi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ndidzakuwira Moabu; inde, ndidzapfuulira Moabu yense, adzalirira anthu a ku Kirere.